Genesis 25:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Isaki anali ndi zaka 40 pamene anakwatira Rabeka, mwana wa Betuele+ wa Chiaramu, wa ku Padani-aramu, amene anali mchemwali wake wa Labani wa Chiaramu. Genesis 25:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pambuyo pake, mʼbale wake anabadwa, ndipo dzanja lake linali litagwira chidendene cha Esau.+ Choncho Isaki anapatsa mwanayo dzina lakuti Yakobo.*+ Pamene Rabeka ankabereka anawa nʼkuti Isaki ali ndi zaka 60.
20 Isaki anali ndi zaka 40 pamene anakwatira Rabeka, mwana wa Betuele+ wa Chiaramu, wa ku Padani-aramu, amene anali mchemwali wake wa Labani wa Chiaramu.
26 Pambuyo pake, mʼbale wake anabadwa, ndipo dzanja lake linali litagwira chidendene cha Esau.+ Choncho Isaki anapatsa mwanayo dzina lakuti Yakobo.*+ Pamene Rabeka ankabereka anawa nʼkuti Isaki ali ndi zaka 60.