Genesis 36:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mayina a ana a Esau ndi awa: Elifazi, mwana wamwamuna amene Ada mkazi wake wa Esau anabereka, komanso Reueli, mwana wamwamuna amene Basemati mkazi wake wa Esau anabereka.+
10 Mayina a ana a Esau ndi awa: Elifazi, mwana wamwamuna amene Ada mkazi wake wa Esau anabereka, komanso Reueli, mwana wamwamuna amene Basemati mkazi wake wa Esau anabereka.+