Genesis 27:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Koma Isaki bambo ake anamuuza kuti: “Taona, udzakhala kutali ndi nthaka yachonde, komanso kutali ndi mame akumwamba.+ Genesis 32:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno Yakobo anatuma anthu kuti apite kwa mchimwene wake Esau, kudziko la Seiri,+ mʼdera la Edomu.+
39 Koma Isaki bambo ake anamuuza kuti: “Taona, udzakhala kutali ndi nthaka yachonde, komanso kutali ndi mame akumwamba.+
3 Ndiyeno Yakobo anatuma anthu kuti apite kwa mchimwene wake Esau, kudziko la Seiri,+ mʼdera la Edomu.+