Ekisodo 28:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ulankhule ndi anthu onse aluso* amene ndinawapatsa mzimu wa nzeru.+ Anthuwo amupangire Aroni zovala zomwe zizisonyeza kuti wayeretsedwa, kuti atumikire monga wansembe wanga. Ekisodo 35:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Anthu onse aluso*+ pakati panu abwere ndipo adzapange zinthu zonse zimene Yehova walamula.
3 Ulankhule ndi anthu onse aluso* amene ndinawapatsa mzimu wa nzeru.+ Anthuwo amupangire Aroni zovala zomwe zizisonyeza kuti wayeretsedwa, kuti atumikire monga wansembe wanga.