Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 4:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Choncho anatumiza anthu ku Silo kukatenga likasa la pangano la Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, amene amakhala pamwamba* pa akerubi.+ Ana awiri a Eli, Hofeni ndi Pinihasi,+ analinso komweko limodzi ndi likasa la pangano la Mulungu woona.

  • Salimo 80:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 80 Inu Mʼbusa wa Isiraeli, mvetserani,

      Inu amene mukutsogolera Yosefe ngati gulu la nkhosa.+

      Inu amene mwakhala pampando wachifumu pamwamba* pa akerubi,+

      Onetsani kuwala kwanu.*

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena