Numeri 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pa tsiku limene Mose anamaliza kumanga chihema,+ anachidzoza+ nʼkuchipatula, limodzi ndi zipangizo zake zonse, guwa lansembe ndi ziwiya zake zonse.+ Atamaliza kudzoza ndi kupatula zinthu zimenezi,+
7 Pa tsiku limene Mose anamaliza kumanga chihema,+ anachidzoza+ nʼkuchipatula, limodzi ndi zipangizo zake zonse, guwa lansembe ndi ziwiya zake zonse.+ Atamaliza kudzoza ndi kupatula zinthu zimenezi,+