Ekisodo 26:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Uike tebulo kunja kwa katani. Uikekonso choikapo nyale+ moyangʼanizana ndi tebulo kumbali yakumʼmwera ya chihemacho. Koma tebulolo uliike mbali yakumpoto.
35 Uike tebulo kunja kwa katani. Uikekonso choikapo nyale+ moyangʼanizana ndi tebulo kumbali yakumʼmwera ya chihemacho. Koma tebulolo uliike mbali yakumpoto.