Ekisodo 36:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kenako anapanga zitsulo 40 zasiliva zokhazikapo mafelemu 20 aja. Zitsulo ziwiri anaziika pansi pa felemu lililonse ndipo munalowa zolumikizira ziwiri.+
24 Kenako anapanga zitsulo 40 zasiliva zokhazikapo mafelemu 20 aja. Zitsulo ziwiri anaziika pansi pa felemu lililonse ndipo munalowa zolumikizira ziwiri.+