Ekisodo 37:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anapanganso ndodo zonyamulira za mtengo wa mthethe ndipo anazikuta ndi golide.+ 1 Mafumu 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mitengo yonyamulirayo+ inali yaitali moti nsonga zake zinkaonekera ku Malo Oyera kutsogolo kwa chipinda chamkati, koma sizinkaonekera panja. Mitengoyo idakali pomwepo mpaka lero.
8 Mitengo yonyamulirayo+ inali yaitali moti nsonga zake zinkaonekera ku Malo Oyera kutsogolo kwa chipinda chamkati, koma sizinkaonekera panja. Mitengoyo idakali pomwepo mpaka lero.