Ekisodo 30:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Upange beseni losambira lakopa+ ndi choikapo chake. Ukatero uliike pakati pa chihema chokumanako ndi guwa lansembe ndipo uthiremo madzi.+
18 “Upange beseni losambira lakopa+ ndi choikapo chake. Ukatero uliike pakati pa chihema chokumanako ndi guwa lansembe ndipo uthiremo madzi.+