Ekisodo 30:18, 19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Upange beseni losambira lakopa+ ndi choikapo chake. Ukatero uliike pakati pa chihema chokumanako ndi guwa lansembe ndipo uthiremo madzi.+ 19 Aroni ndi ana ake azisamba mʼmanja ndi mapazi awo pamenepo.+
18 “Upange beseni losambira lakopa+ ndi choikapo chake. Ukatero uliike pakati pa chihema chokumanako ndi guwa lansembe ndipo uthiremo madzi.+ 19 Aroni ndi ana ake azisamba mʼmanja ndi mapazi awo pamenepo.+