Ekisodo 16:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pa tsiku la 6, anthuwo anatola muyezo wowirikiza kawiri,+ munthu aliyense maomeri awiri. Ndiyeno atsogoleri onse a gulu la Aisiraeli anabwera kwa Mose kudzanena.
22 Pa tsiku la 6, anthuwo anatola muyezo wowirikiza kawiri,+ munthu aliyense maomeri awiri. Ndiyeno atsogoleri onse a gulu la Aisiraeli anabwera kwa Mose kudzanena.