Numeri 21:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho anthuwo anapita kwa Mose nʼkumuuza kuti: “Tachimwa ife chifukwa cholankhula modandaula potsutsana ndi Yehova ndiponso inuyo.+ Tipepesereni kwa Yehova kuti atichotsere njokazi.” Zitatero Mose anawapepesera kwa Mulungu.+ 1 Samueli 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova anauza Samueli kuti: “Mvera zonse zimene anthuwo akuuza, chifukwatu sanakane iwe koma akana ine kuti ndikhale mfumu yawo.+
7 Choncho anthuwo anapita kwa Mose nʼkumuuza kuti: “Tachimwa ife chifukwa cholankhula modandaula potsutsana ndi Yehova ndiponso inuyo.+ Tipepesereni kwa Yehova kuti atichotsere njokazi.” Zitatero Mose anawapepesera kwa Mulungu.+
7 Yehova anauza Samueli kuti: “Mvera zonse zimene anthuwo akuuza, chifukwatu sanakane iwe koma akana ine kuti ndikhale mfumu yawo.+