Ekisodo 13:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pofuna kuwatsogolera, Yehova ankayenda patsogolo pawo. Masana ankawatsogolera pogwiritsa ntchito chipilala cha mtambo+ ndipo usiku ankawatsogolera pogwiritsa ntchito chipilala cha moto kuti chiziwaunikira. Choncho ankatha kuyenda masana komanso usiku.+ Numeri 16:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kora atasonkhanitsa anthu onse omutsatira+ kuti atsutsane nawo pakhomo la chihema chokumanako, ulemerero wa Yehova unaonekera ku gulu lonselo.+ Mateyu 17:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mawu ake adakali mʼkamwa, mtambo wowala kwambiri unawaphimba ndipo panamveka mawu kuchokera mumtambomo akuti: “Uyu ndi Mwana wanga wokondedwa, amene amandisangalatsa kwambiri.+ Muzimumvera.”+
21 Pofuna kuwatsogolera, Yehova ankayenda patsogolo pawo. Masana ankawatsogolera pogwiritsa ntchito chipilala cha mtambo+ ndipo usiku ankawatsogolera pogwiritsa ntchito chipilala cha moto kuti chiziwaunikira. Choncho ankatha kuyenda masana komanso usiku.+
19 Kora atasonkhanitsa anthu onse omutsatira+ kuti atsutsane nawo pakhomo la chihema chokumanako, ulemerero wa Yehova unaonekera ku gulu lonselo.+
5 Mawu ake adakali mʼkamwa, mtambo wowala kwambiri unawaphimba ndipo panamveka mawu kuchokera mumtambomo akuti: “Uyu ndi Mwana wanga wokondedwa, amene amandisangalatsa kwambiri.+ Muzimumvera.”+