Ekisodo 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako Mulungu anati: “Ukachite zimenezi kuti akakhulupirire kuti Yehova Mulungu wa makolo awo, Mulungu wa Abulahamu, Mulungu wa Isaki ndi Mulungu wa Yakobo,+ anaonekera kwa iwe.”+ Ekisodo 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho ndidzakutengani kuti mukhale anthu anga, ndipo ine ndidzakhala Mulungu wanu.+ Inuyo mudzadziwadi kuti ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndikukupulumutsani ku ntchito yokakamiza imene Aiguputo akukugwiritsani.
5 Kenako Mulungu anati: “Ukachite zimenezi kuti akakhulupirire kuti Yehova Mulungu wa makolo awo, Mulungu wa Abulahamu, Mulungu wa Isaki ndi Mulungu wa Yakobo,+ anaonekera kwa iwe.”+
7 Choncho ndidzakutengani kuti mukhale anthu anga, ndipo ine ndidzakhala Mulungu wanu.+ Inuyo mudzadziwadi kuti ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndikukupulumutsani ku ntchito yokakamiza imene Aiguputo akukugwiritsani.