Numeri 14:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Komabe anthu onse amene aona ulemerero wanga ndi zizindikiro zanga+ zimene ndinachita ku Iguputo, komanso zimene ndachita mʼchipululu, koma apitiriza kundiyesa+ maulendo 10 onsewa, ndipo sanamvere mawu anga,+ Salimo 78:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iwo anayesa Mulungu mʼmitima yawo+Pomuumiriza kuti awapatse chakudya chimene ankalakalaka. Salimo 78:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chifukwa chakuti sanakhulupirire Mulungu.+Sanakhulupirire kuti iye angathe kuwapulumutsa. Salimo 106:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iwo anasonyeza mtima wadyera mʼchipululu,+Ndipo anayesa Mulungu mʼchipululumo.+
22 Komabe anthu onse amene aona ulemerero wanga ndi zizindikiro zanga+ zimene ndinachita ku Iguputo, komanso zimene ndachita mʼchipululu, koma apitiriza kundiyesa+ maulendo 10 onsewa, ndipo sanamvere mawu anga,+