1 Samueli 15:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Sauli anayankha Samueli kuti: “Komatu ndamvera mawu a Yehova. Ndagwira ntchito imene Yehova anandituma ndipo ndabweretsa Agagi mfumu ya Amaleki, koma Aamalekiwo ndawapha.+ Esitere 9:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Izi zinali choncho chifukwa Hamani+ mwana wa Hamedata, mbadwa ya Agagi,+ amene ankadana ndi Ayuda onse, anawakonzera Ayudawo chiwembu kuti awaphe.+ Ndiponso iye anachita Puri+ kapena kuti maere, nʼcholinga choti awasokoneze maganizo nʼkuwapha.
20 Sauli anayankha Samueli kuti: “Komatu ndamvera mawu a Yehova. Ndagwira ntchito imene Yehova anandituma ndipo ndabweretsa Agagi mfumu ya Amaleki, koma Aamalekiwo ndawapha.+
24 Izi zinali choncho chifukwa Hamani+ mwana wa Hamedata, mbadwa ya Agagi,+ amene ankadana ndi Ayuda onse, anawakonzera Ayudawo chiwembu kuti awaphe.+ Ndiponso iye anachita Puri+ kapena kuti maere, nʼcholinga choti awasokoneze maganizo nʼkuwapha.