1 Mafumu 8:53 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 Chifukwa munawasankha pakati pa mitundu yonse ya anthu apadziko lapansi+ kuti akhale cholowa chanu ngati mmene munanenera kudzera mwa Mose mtumiki wanu, pamene munkatulutsa makolo athu mu Iguputo, inu Yehova Ambuye Wamkulu Koposa.” Salimo 135:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ya wasankha Yakobo kuti akhale wake,Wasankha Isiraeli kuti akhale chuma chake chapadera.*+
53 Chifukwa munawasankha pakati pa mitundu yonse ya anthu apadziko lapansi+ kuti akhale cholowa chanu ngati mmene munanenera kudzera mwa Mose mtumiki wanu, pamene munkatulutsa makolo athu mu Iguputo, inu Yehova Ambuye Wamkulu Koposa.”