Ekisodo 20:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno anthu onse ankamva mabingu ndi kulira kwa lipenga la nyanga ya nkhosa, ankaona kungʼanima kwa mphezi ndiponso phiri likufuka utsi. Anthuwo atamva komanso kuona zimenezi ananjenjemera ndipo anaima patali.+
18 Ndiyeno anthu onse ankamva mabingu ndi kulira kwa lipenga la nyanga ya nkhosa, ankaona kungʼanima kwa mphezi ndiponso phiri likufuka utsi. Anthuwo atamva komanso kuona zimenezi ananjenjemera ndipo anaima patali.+