Genesis 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pofika tsiku la 7, Mulungu anali atamaliza ntchito imene ankagwira. Pa tsiku la 7 limeneli, iye anayamba kupuma pa ntchito yonse imene ankagwira.+
2 Pofika tsiku la 7, Mulungu anali atamaliza ntchito imene ankagwira. Pa tsiku la 7 limeneli, iye anayamba kupuma pa ntchito yonse imene ankagwira.+