Ekisodo 21:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Munthu amene wamenya bambo ake kapena mayi ake aziphedwa.+ Levitiko 19:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Aliyense wa inu azilemekeza* mayi ndi bambo ake,+ ndipo muzisunga masabata anga.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu. Miyambo 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mwana wanga, uzimvera malangizo a bambo ako,+Ndipo usasiye kutsatira malangizo* a mayi ako.+
3 Aliyense wa inu azilemekeza* mayi ndi bambo ake,+ ndipo muzisunga masabata anga.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu.