Deuteronomo 16:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Musamakhotetse chilungamo,+ musamakondere+ kapena kulandira chiphuphu, chifukwa chiphuphu chimachititsa khungu maso a anthu anzeru+ komanso kupotoza mawu a anthu olungama. 2 Mbiri 19:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Muziopa Yehova+ ndipo muzisamala pochita zinthu, chifukwa Yehova Mulungu wathu si wopanda chilungamo+ kapena watsankho,+ ndipo salandira chiphuphu.”+
19 Musamakhotetse chilungamo,+ musamakondere+ kapena kulandira chiphuphu, chifukwa chiphuphu chimachititsa khungu maso a anthu anzeru+ komanso kupotoza mawu a anthu olungama.
7 Muziopa Yehova+ ndipo muzisamala pochita zinthu, chifukwa Yehova Mulungu wathu si wopanda chilungamo+ kapena watsankho,+ ndipo salandira chiphuphu.”+