Deuteronomo 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Inu mudzakhala odalitsika kwambiri mwa anthu onse.+ Pakati panu sipadzapezeka mwamuna, mkazi kapena chiweto chosabereka.+ Deuteronomo 28:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ana anu+ adzakhala odalitsika* komanso chipatso cha mʼdziko lanu, ana a ziweto zanu, ana a ngʼombe zanu ndi ana a nkhosa zanu adzakhala odalitsika.+
14 Inu mudzakhala odalitsika kwambiri mwa anthu onse.+ Pakati panu sipadzapezeka mwamuna, mkazi kapena chiweto chosabereka.+
4 Ana anu+ adzakhala odalitsika* komanso chipatso cha mʼdziko lanu, ana a ziweto zanu, ana a ngʼombe zanu ndi ana a nkhosa zanu adzakhala odalitsika.+