Oweruza 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Fuko la Yuda litapita, Yehova anapereka Akanani ndi Aperezi mʼmanja mwawo,+ moti anagonjetsa amuna 10,000 ku Bezeki. Oweruza 11:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Zitatero, Yehova Mulungu wa Isiraeli anapereka Sihoni ndi anthu ake onse mʼmanja mwa Aisiraeli. Choncho anawagonjetsa nʼkutenga dziko lonse la Aamori okhala kumeneko.+
4 Fuko la Yuda litapita, Yehova anapereka Akanani ndi Aperezi mʼmanja mwawo,+ moti anagonjetsa amuna 10,000 ku Bezeki.
21 Zitatero, Yehova Mulungu wa Isiraeli anapereka Sihoni ndi anthu ake onse mʼmanja mwa Aisiraeli. Choncho anawagonjetsa nʼkutenga dziko lonse la Aamori okhala kumeneko.+