1 Mafumu 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho mapiko a akerubiwo anali pamwamba pa Likasa, moti akerubiwo anatchinga pamwamba pa Likasalo ndi mitengo yake yonyamulira.+ 1 Mbiri 28:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Anamuuzanso za kulemera kwa golide woyengedwa bwino wa guwa lansembe la zofukiza+ ndiponso golide wa chifaniziro cha galeta,+ kutanthauza akerubi+ agolide otambasula mapiko awo kuphimba likasa la pangano la Yehova.
7 Choncho mapiko a akerubiwo anali pamwamba pa Likasa, moti akerubiwo anatchinga pamwamba pa Likasalo ndi mitengo yake yonyamulira.+
18 Anamuuzanso za kulemera kwa golide woyengedwa bwino wa guwa lansembe la zofukiza+ ndiponso golide wa chifaniziro cha galeta,+ kutanthauza akerubi+ agolide otambasula mapiko awo kuphimba likasa la pangano la Yehova.