-
Ekisodo 39:33, 34Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
33 Kenako anabweretsa kwa Mose chihema+ ndi zipangizo zake zonse, nsalu yake yophimba pamwamba,+ ngowe zake,+ mafelemu ake,+ ndodo zake+ zonyamulira, zipilala zake ndi zitsulo zoika pansi.+ 34 Anabweretsanso chophimba chihemacho cha zikopa za nkhosa zonyika mu utoto wofiira,+ chophimba chinanso chapamwamba pake cha chikopa cha akatumbu, katani,+
-