Ekisodo 40:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndiyeno anaika guwa lansembe zopsereza+ pakhomo la chihema kapena kuti chihema chokumanako, kuti aziperekerapo nsembe yopsereza+ ndi nsembe yambewu, mogwirizana ndi zimene Yehova analamula Mose. 2 Mbiri 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno anapanga guwa lansembe lakopa.*+ Guwalo linali lalikulu mikono 20 mulitali, mikono 20 mulifupi ndipo kuchokera pansi kufika pamwamba linali lalitali mikono 10. Aheberi 13:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ife tili ndi guwa lansembe limene ochita utumiki wopatulika kuchihema alibe ulamuliro wodya zapaguwapo.+
29 Ndiyeno anaika guwa lansembe zopsereza+ pakhomo la chihema kapena kuti chihema chokumanako, kuti aziperekerapo nsembe yopsereza+ ndi nsembe yambewu, mogwirizana ndi zimene Yehova analamula Mose.
4 Ndiyeno anapanga guwa lansembe lakopa.*+ Guwalo linali lalikulu mikono 20 mulitali, mikono 20 mulifupi ndipo kuchokera pansi kufika pamwamba linali lalitali mikono 10.
10 Ife tili ndi guwa lansembe limene ochita utumiki wopatulika kuchihema alibe ulamuliro wodya zapaguwapo.+