Levitiko 4:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndiyeno wansembe azitenga ena mwa magazi a nsembe yamachimoyo ndi chala chake nʼkuwapaka panyanga+ za guwa lansembe zopsereza. Magazi ena onse a mbuziyo aziwathira pansi pa guwa lansembe zopsereza.+
25 Ndiyeno wansembe azitenga ena mwa magazi a nsembe yamachimoyo ndi chala chake nʼkuwapaka panyanga+ za guwa lansembe zopsereza. Magazi ena onse a mbuziyo aziwathira pansi pa guwa lansembe zopsereza.+