-
1 Mafumu 7:45Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
45 ndowa, mafosholo, mbale zolowa ndi ziwiya zina zonse. Hiramu anapanga zinthu zimenezi ndi kopa wonyezimira kuti Mfumu Solomo aziike mʼnyumba ya Yehova.
-