Ekisodo 40:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako udzatchinge bwalo la chihema+ ndi mpanda ndipo pakhomo pa bwalolo udzaikepo nsalu yake yotchinga.+ 1 Mafumu 6:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Anamanga bwalo lamkati+ la mizere itatu ya miyala yosema komanso mzere umodzi wa matabwa a mkungudza.+
8 Kenako udzatchinge bwalo la chihema+ ndi mpanda ndipo pakhomo pa bwalolo udzaikepo nsalu yake yotchinga.+
36 Anamanga bwalo lamkati+ la mizere itatu ya miyala yosema komanso mzere umodzi wa matabwa a mkungudza.+