Ekisodo 39:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Kenako anabweretsa kwa Mose chihema+ ndi zipangizo zake zonse, nsalu yake yophimba pamwamba,+ ngowe zake,+ mafelemu ake,+ ndodo zake+ zonyamulira, zipilala zake ndi zitsulo zoika pansi.+ Ekisodo 39:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Anabweretsanso nsalu zotchingira bwalo, zipilala ndi zitsulo zokhazikapo zipilalazo,+ nsalu yotchinga+ pakhomo la bwalo, zikhomo za bwalo ndi zingwe zake,+ ziwiya zonse zogwiritsa ntchito pa utumiki wapachihema, kapena kuti chihema chokumanako,
33 Kenako anabweretsa kwa Mose chihema+ ndi zipangizo zake zonse, nsalu yake yophimba pamwamba,+ ngowe zake,+ mafelemu ake,+ ndodo zake+ zonyamulira, zipilala zake ndi zitsulo zoika pansi.+
40 Anabweretsanso nsalu zotchingira bwalo, zipilala ndi zitsulo zokhazikapo zipilalazo,+ nsalu yotchinga+ pakhomo la bwalo, zikhomo za bwalo ndi zingwe zake,+ ziwiya zonse zogwiritsa ntchito pa utumiki wapachihema, kapena kuti chihema chokumanako,