Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 39:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Kenako anabweretsa kwa Mose chihema+ ndi zipangizo zake zonse, nsalu yake yophimba pamwamba,+ ngowe zake,+ mafelemu ake,+ ndodo zake+ zonyamulira, zipilala zake ndi zitsulo zoika pansi.+

  • Ekisodo 39:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Anabweretsanso choikapo nyale chagolide woyenga bwino, nyale zake+ zondandalikidwa bwino, ziwiya zonse za choikapo nyalecho,+ mafuta a nyale,+

  • Levitiko 24:1-3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Yehova anapitiriza kulankhula ndi Mose kuti: 2 “Lamula Aisiraeli kuti akubweretsere mafuta ounikira oyenga bwino kwambiri a maolivi, kuti nyale ziziyaka nthawi zonse.+ 3 Aroni azikhazika nyale kunja kwa katani ya Malo Oyera Koposa mʼchihema chokumanako. Nyalezo ziziunikira pamaso pa Yehova nthawi zonse kuyambira madzulo mpaka mʼmawa. Limeneli ndi lamulo kwa inu mpaka kalekale mʼmibadwo yanu yonse.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena