Levitiko 8:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho Mose anaitana Aroni ndi ana ake nʼkuwasambitsa ndi madzi.+ Aheberi 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 tiyeni tifike kwa Mulungu ndi mtima wonse komanso tili ndi chikhulupiriro chonse, chifukwa mitima yathu yayeretsedwa* kuti tisakhalenso ndi chikumbumtima choipa,+ ndipo matupi athu asambitsidwa mʼmadzi oyera.+
22 tiyeni tifike kwa Mulungu ndi mtima wonse komanso tili ndi chikhulupiriro chonse, chifukwa mitima yathu yayeretsedwa* kuti tisakhalenso ndi chikumbumtima choipa,+ ndipo matupi athu asambitsidwa mʼmadzi oyera.+