Levitiko 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndiyeno azitsuka matumbo komanso ziboda ndi madzi. Kenako wansembe aziwotcha nyama yonse kuti paguwa lansembe pakhale utsi, ndipo ikhale nsembe yopsereza. Imeneyi ndi nsembe yowotcha pamoto yakafungo kosangalatsa* yoperekedwa kwa Yehova.
13 Ndiyeno azitsuka matumbo komanso ziboda ndi madzi. Kenako wansembe aziwotcha nyama yonse kuti paguwa lansembe pakhale utsi, ndipo ikhale nsembe yopsereza. Imeneyi ndi nsembe yowotcha pamoto yakafungo kosangalatsa* yoperekedwa kwa Yehova.