-
Levitiko 3:9, 10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Ndipo pansembe yamgwirizanoyo azitengapo mafuta ake ndi kuwapereka kwa Yehova+ monga nsembe yowotcha pamoto. Azichotsa mchira wonse wamafuta pafupi ndi fupa la msana ndiponso mafuta okuta matumbo ndi mafuta onse amene ali pamatumbo. 10 Azichotsanso impso ziwiri zomwe zili pafupi ndi chiuno ndi mafuta okuta impsozo. Komanso azichotsa mafuta apachiwindi pamodzi ndi impsozo.+
-