Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 7:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Ine ndikutenga chidale cha nsembe yoyendetsa uku ndi uku ndiponso mwendo womwe ndi gawo lopatulika. Ndikutenga zimenezi pansembe zamgwirizano za Aisiraeli nʼkuzipereka kwa Aroni wansembe ndi ana ake. Limeneli ndi lamulo kwa Aisiraeli mpaka kalekale.+

  • Levitiko 10:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Mudyenso chidale cha nsembe yoyendetsa uku ndi uku ndi mwendo wa gawo lopatulika.+ Muzidyere pamalo amene ayeretsedwa, inuyo, ana anu aamuna ndi ana anu aakazi.+ Muzichita zimenezi chifukwa zinthu zimenezi zaperekedwa kwa inu monga gawo lanu ndi gawo la ana anu kuchokera pa nsembe zamgwirizano za Aisiraeli.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena