-
Levitiko 22:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Iwo azisunga malamulo anga kuti asachimwe nʼkufa chifukwa chodetsa zinthu zopatulika atalephera kusunga malamulowo. Ine ndine Yehova amene ndikuwayeretsa.
-