Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 32:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Mose atayandikira msasawo nʼkuona mwana wa ngʼombe+ ndi anthu akuvina, mkwiyo wake unayaka ndipo anaponya pansi miyala ija nʼkuiswa ali mʼmunsi mwa phiri.+

  • Deuteronomo 9:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Choncho ndinatenga miyala iwiriyo nʼkuiponya pansi mwamphamvu ndi manja anga, ndipo ndinaiswa inu mukuona.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena