-
Aroma 2:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Tikudziwa kuti Mulungu akamaweruza anthu amene amachita zimenezi kuti ndi oyenera kulandira chilango, amawaweruza mogwirizana ndi choonadi.
-