Ekisodo 22:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ngati munthu wapatsa mnzake ndalama kapena katundu wina kuti amusungire, zinthuzo nʼkubedwa mʼnyumba ya mnzakeyo, wakubayo akapezeka azilipira zowirikiza kawiri.+ Levitiko 19:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Musamabe,+ musamapusitse anzanu+ ndiponso musamachitirane chinyengo.
7 Ngati munthu wapatsa mnzake ndalama kapena katundu wina kuti amusungire, zinthuzo nʼkubedwa mʼnyumba ya mnzakeyo, wakubayo akapezeka azilipira zowirikiza kawiri.+