Ekisodo 28:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Zovala zoti apange ndi izi: chovala pachifuwa,+ efodi,+ malaya akunja odula manja,+ mkanjo wamandalasi, nduwira+ ndi lamba wapamimba.+ Aroni mʼbale wako ndi ana ake awapangire zovala zopatulikazi, kuti atumikire monga ansembe anga. Ekisodo 39:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Kenako anabweretsa kwa Mose chihema+ ndi zipangizo zake zonse, nsalu yake yophimba pamwamba,+ ngowe zake,+ mafelemu ake,+ ndodo zake+ zonyamulira, zipilala zake ndi zitsulo zoika pansi.+ Ekisodo 39:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 zovala zolukidwa bwino zoti azivala potumikira mʼmalo opatulika, zovala zopatulika za Aroni wansembe+ ndi zovala za ana ake zoti azivala potumikira monga ansembe.
4 Zovala zoti apange ndi izi: chovala pachifuwa,+ efodi,+ malaya akunja odula manja,+ mkanjo wamandalasi, nduwira+ ndi lamba wapamimba.+ Aroni mʼbale wako ndi ana ake awapangire zovala zopatulikazi, kuti atumikire monga ansembe anga.
33 Kenako anabweretsa kwa Mose chihema+ ndi zipangizo zake zonse, nsalu yake yophimba pamwamba,+ ngowe zake,+ mafelemu ake,+ ndodo zake+ zonyamulira, zipilala zake ndi zitsulo zoika pansi.+
41 zovala zolukidwa bwino zoti azivala potumikira mʼmalo opatulika, zovala zopatulika za Aroni wansembe+ ndi zovala za ana ake zoti azivala potumikira monga ansembe.