Ekisodo 28:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Uuze munthu waluso lopeta kuti apange chovala pachifuwa chachiweruzo+ ndipo achipange mwaluso mofanana ndi efodi. Achipange ndi golide, ulusi wabuluu, ubweya wa nkhosa wapepo, ulusi wofiira kwambiri ndi ulusi wopota wabwino kwambiri.+ Ekisodo 39:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Akachipinda pakati chinali chofanana mbali zonse 4. Chovala pachifuwacho anachipanga kuti akachipinda pakati, mulitali mwake chizikhala masentimita 22* ndiponso mulifupi mwake masentimita 22.
15 Uuze munthu waluso lopeta kuti apange chovala pachifuwa chachiweruzo+ ndipo achipange mwaluso mofanana ndi efodi. Achipange ndi golide, ulusi wabuluu, ubweya wa nkhosa wapepo, ulusi wofiira kwambiri ndi ulusi wopota wabwino kwambiri.+
9 Akachipinda pakati chinali chofanana mbali zonse 4. Chovala pachifuwacho anachipanga kuti akachipinda pakati, mulitali mwake chizikhala masentimita 22* ndiponso mulifupi mwake masentimita 22.