Ekisodo 28:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Upangenso kachitsulo konyezimira kagolide woyenga bwino ndipo ulembepo mochita kugoba ngati mmene amagobera chidindo, mawu akuti: ‘Yehova ndi Woyera.’+ Ekisodo 39:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Atatero anapanga kachitsulo konyezimira kagolide woyenga bwino, chizindikiro chopatulika cha kudzipereka. Analembapo mawu akuti: “Yehova ndi Woyera.” Mawuwa anawalemba mochita kugoba ngati mmene amagobera chidindo.+
36 Upangenso kachitsulo konyezimira kagolide woyenga bwino ndipo ulembepo mochita kugoba ngati mmene amagobera chidindo, mawu akuti: ‘Yehova ndi Woyera.’+
30 Atatero anapanga kachitsulo konyezimira kagolide woyenga bwino, chizindikiro chopatulika cha kudzipereka. Analembapo mawu akuti: “Yehova ndi Woyera.” Mawuwa anawalemba mochita kugoba ngati mmene amagobera chidindo.+