8 Kenako azichotsa mafuta onse a ngʼombe ya nsembe yamachimo, kuphatikizapo mafuta okuta matumbo ndi mafuta onse apamatumbo. 9 Azichotsanso impso ziwiri zomwe zili pafupi ndi chiuno ndi mafuta okuta impsozo. Komanso azichotsa mafuta apachiwindi pamodzi ndi impsozo.+