Ekisodo 29:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndiyeno utengeko magazi amene ali paguwa lansembe ndi mafuta pangʼono odzozera+ nʼkuwadontheza pa Aroni ndi pazovala zake. Uwadonthezenso pa ana ake ndi zovala zawo kuti Aroni ndi zovala zake ndiponso ana ake ndi zovala zawo akhale oyera.+
21 Ndiyeno utengeko magazi amene ali paguwa lansembe ndi mafuta pangʼono odzozera+ nʼkuwadontheza pa Aroni ndi pazovala zake. Uwadonthezenso pa ana ake ndi zovala zawo kuti Aroni ndi zovala zake ndiponso ana ake ndi zovala zawo akhale oyera.+