Levitiko 6:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndipo chiwiya chadothi chimene mungawiritsiremo nyamayo muzichiswa. Koma mukawiritsira mʼchiwiya chakopa,* muzichikwecha nʼkuchitsuka ndi madzi.
28 Ndipo chiwiya chadothi chimene mungawiritsiremo nyamayo muzichiswa. Koma mukawiritsira mʼchiwiya chakopa,* muzichikwecha nʼkuchitsuka ndi madzi.