Ekisodo 29:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Uzipereka ngʼombe ya nsembe yamachimo tsiku lililonse kuti iphimbe machimo. Uziyeretsa guwa lansembe ku machimo poliperekera nsembe yophimba machimo, ndipo uzilidzoza kuti likhale loyera.+ Levitiko 17:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chifukwa moyo wa nyama uli mʼmagazi+ ndipo ine ndawapereka paguwa lansembe+ kuti azikuphimbirani machimo. Zili choncho chifukwa magazi ndi amene amaphimba machimo+ chifukwa cha moyo umene uli mʼmagaziwo.
36 Uzipereka ngʼombe ya nsembe yamachimo tsiku lililonse kuti iphimbe machimo. Uziyeretsa guwa lansembe ku machimo poliperekera nsembe yophimba machimo, ndipo uzilidzoza kuti likhale loyera.+
11 Chifukwa moyo wa nyama uli mʼmagazi+ ndipo ine ndawapereka paguwa lansembe+ kuti azikuphimbirani machimo. Zili choncho chifukwa magazi ndi amene amaphimba machimo+ chifukwa cha moyo umene uli mʼmagaziwo.