Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 14:7, 8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Koma musamadye nyama izi zokha zimene zimabzikula kapena zimene zili ndi ziboda zogawanika: ngamila, kalulu ndi mbira, chifukwa zimabzikula koma si zogawanika ziboda. Nyama zimenezi nʼzodetsedwa kwa inu.+ 8 Musamadyenso nkhumba chifukwa ndi ya ziboda zogawanika koma sibzikula. Imeneyi ndi yodetsedwa kwa inu. Musamadye nyama yake kapena kuikhudza ikafa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena