Ekisodo 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho ndidzakutengani kuti mukhale anthu anga, ndipo ine ndidzakhala Mulungu wanu.+ Inuyo mudzadziwadi kuti ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndikukupulumutsani ku ntchito yokakamiza imene Aiguputo akukugwiritsani. Ekisodo 29:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova Mulungu wawo, amene ndinawatulutsa mʼdziko la Iguputo kuti ndikhale pakati pawo.+ Ine ndine Yehova Mulungu wawo.” Hoseya 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Isiraeli ali mnyamata ndinamukonda,+Ndipo ndinaitana mwana wangayu kuti atuluke mu Iguputo.+
7 Choncho ndidzakutengani kuti mukhale anthu anga, ndipo ine ndidzakhala Mulungu wanu.+ Inuyo mudzadziwadi kuti ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndikukupulumutsani ku ntchito yokakamiza imene Aiguputo akukugwiritsani.
46 Iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova Mulungu wawo, amene ndinawatulutsa mʼdziko la Iguputo kuti ndikhale pakati pawo.+ Ine ndine Yehova Mulungu wawo.”