Levitiko 18:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Usayandikire mkazi kuti ugone naye pa nthawi imene akusamba chifukwa ndi wodetsedwa.+ Levitiko 20:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mwamuna akagona ndi mkazi amene akusamba, onse awiri sanalemekeze magazi a mkaziyo.+ Onse awiri aziphedwa kuti asakhalenso pakati pa anthu a mtundu wawo.
18 Mwamuna akagona ndi mkazi amene akusamba, onse awiri sanalemekeze magazi a mkaziyo.+ Onse awiri aziphedwa kuti asakhalenso pakati pa anthu a mtundu wawo.